CREATIVE SOCIETY

Polojekiti yapadziko lonse

Moyo wa munthu ndiye chinthu cha mtengo wapamwamba kwambiri
#creativesociety
CREATIVE SOCIETY ndi ntchito yapadziko lonse yomwe imagwirizanitsa anthu ochokera kumaiko oposa 180 mwaufulu. Cholinga cha polojekitiyi ndikusintha, mwanjira yalamulo komanso mwamtendere pa nthawi yochepa kupita mu dziko latsopano lomwe moyo wa munthu udzakhala ofunikila koposa chilichose.

Kodi Creative Society inayamba bwanji?

Kafukufuku wamkulu kwambiri wazaka zambiri, wochitidwa pazaka khumi, anaulula kufunikira kwenikweni kwa dziko latsopano kwa anthu. Mayankho ochokera kwa anthu mamiliyoni ambiri mmayiko 180 osiyanasiyana adatsimikizira kuti chofunikira kwambiri ndi moyo wa munthu.

Wophunzira aliyense yemwe adafunsidwa mafunso adafunsidwa funso limodzi: "Kodi mukufuna kukhala m'dziko lotani?" Kutengera mayankho, mizati 8 ya Creative Society idapangidwa ndikukhala maziko a dziko latsopanoli. Kuti izi zitheke, anthu ambili akulumikizana ndikutengapo mbali mu polojekitiyi.

Ndani ali kumbuyo kwa Creative Society?

Anthu mamiliyoni ambiri ochokera zikhalidwe zosiyanasiyana, mayiko, zipembedzo, zipembedzo, ndi zikhulupiriro, omwe akufuna kusintha dziko lathu kuti azichita bwino komanso mwa mwamtendere. Tsiku lililonse, kuchuluka kwa anthu otere kumakulirakulira.

Anthu ochokera padziko lonse lapansi, omwe amadzipanga okha komanso kuchita zinthu mosamalitsa pa cholinga chofuna kupanga moyo wabwino kwa anthu onse ndi mibadwo yamtsogolo.

Kodi Ndani amapereka ndala zothandizira kumaga Creative Society?

All actions and activities within the framework of the Creative Society project are carried out solely by the project participants themselves, on their initiative, by their choice and willingness, and at the expense of their own funds.

The Creative Society project does not have bank accounts, finance or property, does not accumulate funds, and does not make any profit.

Creative Society ndi polojekiti yodzipereka kwambiri yoyendera mu chimango chalamulo. Zimangoyimira zokonda za anthu okha m'malo moyang'ana mayiko ena, zipani, kapena mabungwe.

Kodi nchifukwa chiyani tikufunika Creative Society padziko lonse lapansi?

Dziko latsopano a Creative Society likufunka padziko lonse lapansi chifukwa ndi dziko lokhalo
 

lomwe lingapereke njira zothetsera mavuto onse padziko lonse lapansi, kuphatikizapo vuto la nyengo;
lomwe lingawonetsere tsogolo lopanda nkhondo, mikangano, chiwawa, umphawi, kapena njala;
lomwe lipangitse kuti anthu azikhala ndi gawo latsopano la chiyambi chatsopano cha chisinthiko;
Imatsimikizira chitetezo cha munthu aliyense payekhapayekha, thanzi, komanso chitukuko chonse.

Kodi ndizotheka kumanga Creative Society mdziko kapena mgwirizano wamaiko angapo?

Masiku ano, mayiko onse pa dziko lapasi ndiolumikizana komaso odalilana. Pachifukwa ichi, kuyesera kumanga creatve society mu dziko limodzi kapena kupanga mgwilizano wa mayiko angapo ndikosatheka.

Kumanga Creative Society ndikotheka pomwe anthu onse atenga mbali padziko lonse lapansi nthawi yomweyo pa nthawi yosinthira dziko, mayiko atha kungoyankhula kuti akufuna Creative Society, koma ngati dziko kapena kagulu ka mayiko kangasinthe pawokha, chitetezo komaso moyo wa anthu awo udzakhala pachiopsezo ku mayiko omwe sadavomeleze za Creative Society.

Mizati 8 ya Creative Society

The 8 Pillars of the Creative Society are what people from all over the world desire. These are the fundamental values of the Creative Society that can become the basis of international law and legislation in all countries through a lawful expression of people
1.Moyo wa Anthu

Moyo wa munthu ndiye chithu cha mtengo wapamwamba kwambiri. Moyo wa munthu aliyense uyenera kutetezedwa kukhala . Cholinga cha anthu ndikuwonetsetsa kuti atsimikizire kufunika kwa moyo wa munthu aliyense. Palibe ndipo palibe chomwe chingakhale chamtengo wapatali kuposa moyo wa munthu. Ngati munthu m'modzi ndi wofunika, ndiye kuti anthu onse ndi amtengo wapatali!

2.Ufulu waumunthu

Munthu aliyense amabadwa ndi ufulu wokhala munthu wokhalapo. Anthu onse amabadwira ufulu komanso wofanana. Aliyense ali ndi ufulu wosankha. Sipangakhale aliyense komanso palibe chilichonse padziko lapansi kuposa munthu, ufulu wake ndi ufulu wake. Kukhazikitsa kwa ufulu ndi kumasulidwa kwa anthu sikuyenera kuphwanya ufulu ndi ufulu wa ena.

3.Chitetezo cha anthu

Palibe aliyense ndipo palibe chilichonse chomwe chili ndi ufulu wopereka chiopsezoku moyo ndi ufulu wa munthu!

Munthu aliyense amakhala ndi kutsimikizika kwaulere kukhala ndi zofunika pamoyo , kuphatikizapo chakudya, nyumba, chithandizo chamankhwala, maphunziro ndi chitetezo chathunthu.

Zochita zasayansi, zamafakitale komanso zaukadaulo za dziko ziyenera kukhala ndi cholinga chosintha moyo wamunthu.

Zotsimikizika zachuma: opanda kukwera kwa mitengo ya zinthu ndi mavuto ena a zachuma, mitengo yokhazikika komanso yofananaop padziko lonse lapansi, ndalama imodzi, komanso misonkho yokhazikika kapena opanda msonkho.

Chitetezo cha anthu ndi dziko ku zoopsa zilizonse zimatsimikiziridwa ndi mgwirizano wa dziko lonse lapasi yomwe imaona zinthu zadzidzidzi.

4.Kuwonekera ndi kutseguka kwa chidziwitso kwa onse

Munthu aliyense ali ndi ufulu wodziwa zokhudzana ndi kayendedwe ndi kagwiilidwe ntchito ka ndalama zaboma. Munthu aliyense amakhala ndi chidziwitso chokhudza kukhazikitsidwa kwa zisankho za dziko .

Owulutsa nkhani amayimila dziko ndi anthu and amayenera kufalitsa uthenga oona komaso mosabisa.

5.Malingaliro akuya

Malingaliro amayenera kukhala otukula moyo wa anthu ndikuimitsa chilichonse chomwe chogwetsa munthu. Cholinga chachikulu ndicho chinthu chofunikira kwambiri cha anthu, zauzimu komanso zofuna za munthu, umunthu, ulemu ndi kulimbikitsana ndi kulimbikitsa ubwenzi.

Kupanga Makhalidwe olimbikitsa Chitukuko ndi Maphunziro a munthu, kukulitsa makhalidwe anu abwino komanso padziko.

Kuletsa mabodza achiwawa, kutsutsidwa komanso kudzudzula mtundu uliwonse wa magawano, nkhanza zamphamvu, ndi chinyengo.

6.Kukula kwa Umunthu

Munthu aliyense mu creative societ ali ndi ufulu wa chitukuko ndi kukwaniritsidwa zofuna zathu.

Maphunziro ayenera kukhala aulere komanso opezeka kulikose chimodzimodzi. Kupanga makhalidwe ndi kukulitsa mwayi wa munthu kukwaniritsa kuthekera maluso ake.

7.Chilungamo ndi Kufanana

Zinthu zonse zachilengedwe ndi za anthu ndipo zimagawidwa pakati pa anthu onse. kukondera pogawa ndi koletsedwa. Zinthu izi zimagawidwa pakati pa nzika za dziko lonse lapansi.

Munthu ali ufulu okhala pa ntchito yomwe iye akufuna. malipiro ofanana, pa ntchito zofanana dziko lonse lapasi.

Aliyense ali ndi ufulu wokhala ndi katundu payekha ndi ndalama, komabe ali ndi malire a kuchuluka kwa chiwerengero cha chuma chokhazikitsidwa.

8.Dziko lodzilamulira lokha

Lingaliro la “Mphamvu” mu creative society mulibe, popeza udindo wa anthu onse, kukula kwake, makhalidwe ndi mtendere zili mmanja mwa anthu onse.

Aliyense ali ndi ufulu otengapo mbali pa zochitika mu creative society ndikusamala malamulo opititsa patsogolo moyo wa munthu.

Mayankho a mavuto azachikhalidwe, yazachuma, komanso zachuma zomwe zimakhudza moyo wamunthu zimaperekedwa kuti anthu akambilane ndi kuvota (referendum).

Zindikirani za mizati 8
Mu Creative Society, sipadzakhala chifukwa chogwiritsira ntchito ndalama, chifukwa cha kuyambitsa kwa mtundu watsopano wachuma ndi matekinoloje atsopano. Chifukwa chake, ina mwa mizati 8 imakamba zakuti ndalama idzangogwilitsidwa ntchito pa nthawi yosinthira kulowa mu Creative Society.

Kodi Creative Society imapereka chiyani kwa aliyense padziko lapansi?

Creative Society ndi dziko lopereka mwayi waukulu kwa aliyese.
Kuti tikhazikitse Creative Society, tikuyenera kubweretsa ntundu watsopano wa ndalama komaso ukadaulo ndikukozaso machitidwe a zinthu mu mdziko kenako nthawi yakusintha idzafika yomwe idzakhala zaka 5 kapena 6 potengera ndi kuyerekeza kwathu koyamba. Mu nthawi yosinthira, munthu aliyese, pa ufulu wakubadwa adzalandira zabwino zotsatirazi:
Chuma choyambirira cha pamwezi chofanana ndi USD 10,000 kwa aliyense wamkulu;
Kulipira kamodzi kofanana ndi US 100,000 pa kubadwa kwa mwana woyamba, USD 200,000 pa kubadwa kwa Mwana Wachiwiri, ndi zina. Malipiro a pamwezi ogwirizana ndi USD 5,000 kwa mwana aliyense mpaka zaka 6 ndi USD 7,000 kwa mwana wazaka 7 mpaka kukula;
kukhala ndi nyumba za ntengo wapamwamba komanso zabwino zokhala ndi malo osachepera 650 sikweya fiti (mamita 60 sikweya) pamunthu aliyense;
Zaumoyo wapamwamba padziko lonse lapansi, zaulere;
Maphunziro apamwamba kwambiri kulikonse padziko lapansi, kwaulere;
Kugwira ntchito ma ola anayi pa tsiku, masiku anayi pa sabata,kulandila salale yofanana dziko lonse lapasi pa ma udindo ofanana, kupatsidwa tchuthi ya masiku 30 kawili pachaka;
Dziko lotetezedwa lopanda nkhondo, mikangano, upandu, ndi katangale;
Kutsimikizika kwachuma: palibe kuchuluka kwachuma, kusokonekera kwachuma kapena zovuta; mitengo yokhazikika padziko lonse lapansi;
Palibe misonkho ya aliyense payekhapayekha, mabizinesi ang'onoang'ono ndi apakatikati;
Kugwiritsa ntchito kopanda mallire (mpweya, magetsi, kutentha, ndi zina) kwa aliyense payekhapayekha, kwaulere;
Kuchotsa ngongole zonse;
Maulendo aulere ndi mayendedwe opanda malire padziko lonse lapansi;
Kupita patsogolo kwa maukadaulo zopititsa patsogolo moyo wa aliyese kuti azigwilitsa ntchito pa dziko lonse.

Kodi mu Creative Society, zinthuzi zidzapatsidwa bwanji kwa munthu aliyense padziko lonselapansi?

Mu Creative Society, kukhala ndi moyo wapamwamba kudzatsimikiziridwa kwa munthu aliyense padziko lapansi mtundu watsopano wachuma Izi zilibe zofananira m'mbiri ya anthu. Mtunduwu wapangidwa ndikufunsidwa ndi akatswiri padziko lonse lapansi, ndipo zdzasintha moyo wathu kuyambira tsiku loyamba la kukhazikitsa kwake.
Mutha kudziwa zambiri za mtunduwu powona mwatsatanetsatane makanema omwe afotokozedweratu pa forumu “vuto lapadziko lonse lapansi. Pali Njira Yothetsera mavutowa”

Poganizira kuti mu Creative Society, munthu aliyese azidzalandira phindu pakubadwa, nanga chikufunkila ndichani kwa munthu?

Mu Creative Society, munthu amalandira phindu lambiri ndi zabwino. Izi zimafunikira kutenga nawo mbali payekha payekha payekha pazinthu zokhudzana ndi ntchito yawo, zopereka ,zaluntha, ndi luso mu dzikoo. mu Creative Society, anthu azidzadzikwezera miyoyo yawo ndikuthandiza dziko lonse.
Kutenga nawo mbali kwa anthu pazochitika za mdziko ndi zogwirizana ndi malamulo ndi zisankho pa nkhani zofunika kwambiri pamoyo. Izi ndichifukwa chakuti mu Creative Society, ndi dziko lokhalo lomwe ulamulilo sukhala mmaanja mwa munthu mmodzi koma anthu onse dziko lonse lapasi. ziganizo zizidzapangidwa pazisankho.
Chifukwa chake, mu Creative Society, palibe lingaliro la "Mphamvu pa Anthu" Popeza mphamvu zidzapatsidwa kwa aliyense. Anthu pamodzi adzathetsa mavuto onse padziko lonse lapansi komanso mumadera.

Chifukwa chiyani Creative Society suyenera kuyerekezedwa ndi mitundu ina

omwe adakhazikitsidwa kale, komanso kwa iwo omwe adapangidwa kongowaganizira, koma osakwanilitsidwa? Chifukwa chakuti, m'mitundu ina yonse, mphavu zimakhala kwa gulu la anthu ochepa kwambiri kuposa ambiri nthawi zonse mobisika kapena poyera. pomwe mu Creative Society palibe amene adzadzikundikile mphavu kapena kuzichotsa ku anthu chifukwa zidzagawidwa mofanana kwa anthu onse kudzera mu dziko lodzilamulira.

Kuti muve zambiri za dziko lodzilaulira, onelani kanema pa foramu ya dziko lonse ''mavuto a dziko lnse, pali njira yothetsera mavutowa'':

Kodi tingamange bwanji Creative Society padziko lonse lapansi m'zaka zikubwerazi?

Pali njira ziwiri zomangira Creative Society. Magawo onse awiriwa amachitika molingana ndi miyambo komanso malamulo adziko lonse.
1
Gawo Lodziwitsa/ lofalitsa uthenga
Pogwilitsa ntchito ufulu wanu, anthu amadziwitsa ena za Creative Society. Mwanjira imeneyi, kufunikira kovomerezeka komanso kwamtendere kumapangidwa kuti lipange Creative Society padziko lonse lapansi.Anthu ambiiri akangofuna kupanga creative society mwachangu, ndiyekuti tilowa siteji yachiwili yomanga Creative Society mwachangu.
2
Gawo lokonzekera ndi kuchititsa kuti dziko lapansi libwerenso (world referendum)
Anthu ambiri m'maiko onse akadzasapota Creative Society, tidzakozekeretsa kusintha kwa dziko lonse kuti titsatire dziko latsopanoli kuti ndilo lofunikila kuti tikhale ndi moyo wopambana.
Pokonzekera referendum padziko lonse lapansi, maziko aukadaulo adzapangidwa ndikugwilitsidwa ntchito.

Funso lotsatirali lidzaperekedwa pakuvotera padziko lonse lapansi:

Kodi anthu akuvomeleza kusintha dziko kuchoka ku consumerist format kupita ku Creative Society, lomwe likubweletsa anthu tonse dziko lonse lapasi mu dziko limodzi?

Chisankho chabwino chidzapangidwa:

kukhazikitsidwa kwa mizati 8 ya Creative Society idzakhazikitsidwa ngati ngodya ya malamulo a dziko lonse lapasi;

kuvomerezedwa kwa bungwe la zisankho lapadziko lonse lapansi monga Bungwe Lolamulira Padziko Lapansi;

kusankhidwa kwa tsiku loyambira kusintha kupita mu Creative Society.

Chiganizo chabwino chikadzapangidwa pa nthawi yosintha dziko, anthu adzayamba kuonetsera mphavu zawo, a ndale adzakhala okwanilitsa zofuna za anthu onse, zimene zikutanthauza kuti malamulo ndi ziganizo zonse zoyendetsera dziko zizidzapangidwa ndi anthu onse podzila mu zisankho pa bungwe loona za zisankho la dziko lonse lapasi, limene lili lopereka chilolezo cha zinthu zoyenera kutsatira pa moyo wa anthu.

Kodi mungatani kuti muyambe kukhala mu Creative Society posachedwa?

Joinanai mamiliyoni a anthu padziko lonse lapansi omwe akuchita kale ndikudziwitsani mdera lanu, anzanu ndi alendo za Creative Society. Zochita izi ndizofunikira kuti pakhale chilakolako padziko lonse lapasi chomanga Creative Society. Ngati anthu angazindikile mwachangu pa dziko lonse za Creative Society, titha kufika nthawi yosinthira posachedwaapa.

Ngati pa refulendamu ya dziko lonse,anthu ambiri adzafune kusintha dzikoli kupita ku Creative Society mu miyezi 6, Nthawi yosinthira idzafika, malinga ndi mawerengero athu idzatenga zaka 5 kapena 6. Itadzangomalizika, tidzalowa mu dziko latsopano la Creative Society.

Ndikofunika kudziwa kuti zabwino zambiri komanso mwayi udzapezeka kuyambira tsiku loyamba kusintha. Aliyese adzalandila chitetezo, moyo wa mtengo wapatali mwamtendere.

Kodi Ndingatengepo mbali bwanji
mu projekiti ya Creative Society?

Ngati mungafalitse uthenga wacreative society ngakhale kungotsimikizila za kupezeka kwa polojekiti ya Creative Society ndekuti mukutengapo kale mbali.Ngati mukuvomelezana nayo polojekitiyi, falitsani uthenga wake mu dzira zaperekedwa m'musimu.

Pangani logo ya Creative Society:

Kuwona

Kodi mukufuna kudziwitsa aliyense za Creative Society mwachangu komanso mokwanira, kuti ifike posachedwa?

Lowani malo omwe alipo kale (ma CC) m'dera lanu, kapena, ngati kulibe, mutha kutsekula. Izi zithandiza kufalitsa uthengawu mwachangu zimene zingapangitse kumanga Creative Society mwachangu.
Malo anu ogwirizanitsa (CC) amatanthauza kuti anthu omwe angakhale ndi udindo wodziwitsa anthu okhala mnyumba yanu, msewu, mdera lathu, kapena mzinda wonena za Creative Society ndi kuchita modzipereka, mogwirizana ndi malamulo am'deralo.
Ngati mukufuna kulowa nawo mu mgulu la CC lomwe ilipo kapena mukufuna kutsekula lina, chonde tidziwitseni [email protected]

Udindo wa andale
pomanga Creative Society

Andale, kuphatikiza mamembala andale komanso atsogoleri a mayiko, ali ndi mwayi waukulu wodziwitsa za Creative Society chifukwa cha ntchito zawo, maudindo, kufala ndi kutchuka. Kuphatikizidwa kwa andale podziwitsa za Creative Society kudzathandizira kwambiri kumanga Creative Society mwachangu.

Otengapo mbali a Creative Society atha kuthandizila andalewa potsatira malamulo oyenera.

Tiyenera kukumbukira kuti andale omwe amathandizira Creative Society komanso kuchita zinthu zodzipereka za ntchitoyi, ngakhale atakhala ndi mphamvu, zomwe zimathandizidwa ndi malamulo awo, kuphatikizapo amakakamizidwa kuteteza malamulo ndi zokonda za dziko lawo, zofuna za anthu ake, komanso za chipani chawo ngati asankhidwa kukhala oimira ake.

Kuphatikiza apo, andale mdziko lawo komaso pa dziko lonse lapasi ayenera kugwiritsa ntchito njira zovomerezeka zodziwitsa anthu za Creative Society ndikuthandizila kulimanga mwachangu. Kutengera kuthekera kwa dziko lawo, amatha kuphatikiza mizati ina ya Creative Society ku malamulo a dzikolo mothandizidwa ndi anthu, ufulu wawo; ngati siyikuwononga kapena kufooketsa dzikolo pa ndale, chikhalidwe, kapena m'njira ina iliyonse;ngati sapititsa boma kapena kuchititsa kuti dzikolo likhale lolamulira, kudzilamulira komanso kukhulupirika; Simapangitsa kuti dziko likhale locheperako, kapena kupangitsa kuti dzikolo likumane ndi zotsatira zina zovuta.

Dziko lotereli lipitirize kuyanjana ndi mayiko ena omwe amakhalabe mu consumerist fomart omwe ndi osakhulupirika, ankhanza. ali ndi malamulo aupandumchifukwa chake ngati refulelendamu ingafike, dziko lotereli silingakhale lokozeka ngati kugwilitsa ntchito mizati 8 ya Creative Society - kulemekeza moyo wa munthu. Pa nthawi yosinta malamulo, a ndale ali ndi udido otetezera dziko komaso anthu ake.

Nawonso anthu amene amathandizira Creative Society ayenera kutsatira malamulo a dziko lawo ndipo safunika kuakamiza a ndale kubweretsa phindu la Creative Society mu dzikomo zimene zitha kubweretsa mavuto ku anthu ake. Kukwanilitsa ndikubweretsedwa kwa phindu lake la Creative Society lidzabwera pokhapokha tapanga chiganizo chomanga Creative Society pa nthawi yosinthira.

Ndi ubwino uti wina ndi mwayi womwe aliyense adzalandira mu Creative Society?

Mutha kudziwa zambiri za Creative Society pa maforamu apadziko lonse lapansi omwe adamasuliridwa m'zilankhulo 150 za dziko lapansi:
Vuto lapadziko lonse. Kupulumuka Kwathu Kuli mu mgwilizano | Padziko Lonse 12.11.2022
Vuto lapadziko lonse, pali njira yothetsera mavutowa. Msonkhano wa pa intaneti wapadziko lonse 22.04.2023